Settings
Surah The Opening [Al-Fatiha] in Chewa
بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَـٰنِ ٱلرَّحِیمِ ﴿1﴾
M’dzina la Allah Wachifundo chambiri, Wachisoni chosatha.
ٱلۡحَمۡدُ لِلَّهِ رَبِّ ٱلۡعَـٰلَمِینَ ﴿2﴾
Kutamandidwa konse ndi kwa Allah Mbuye wa zolengedwa zonse.
ٱلرَّحۡمَـٰنِ ٱلرَّحِیمِ ﴿3﴾
Wachifundo chambiri, Wachisoni chosatha.
مَـٰلِكِ یَوۡمِ ٱلدِّینِ ﴿4﴾
Mwini tsiku la chiweruziro.
إِیَّاكَ نَعۡبُدُ وَإِیَّاكَ نَسۡتَعِینُ ﴿5﴾
Inu Nokha tikukupembedzani, ndiponso Inu Nokha tikukupemphani chithandizo.
ٱهۡدِنَا ٱلصِّرَ ٰطَ ٱلۡمُسۡتَقِیمَ ﴿6﴾
Tiongolereni kunjira yoongoka.
صِرَ ٰطَ ٱلَّذِینَ أَنۡعَمۡتَ عَلَیۡهِمۡ غَیۡرِ ٱلۡمَغۡضُوبِ عَلَیۡهِمۡ وَلَا ٱلضَّاۤلِّینَ ﴿7﴾
Njira ya omwe mudawapatsa chisomo; osati ya amene adakwiyiridwa (ndi Inu) osatinso ya omwe adasokera.
English
Chinese
Spanish
Portuguese
Russian
Japanese
French
German
Italian
Hindi
Korean
Indonesian
Bengali
Albanian
Bosnian
Dutch
Malayalam
Romanian